Aroma 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, popeza tsopano tayesedwa olungama chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro,+ tiyeni tikhale pa mtendere+ ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu. Aroma 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano adzachita zoposa pamenepo mwa kutipulumutsa ku mkwiyo wake+ kudzera mwa Khristu, popeza tayesedwa olungama kudzera m’magazi a Khristuyo.+
5 Chotero, popeza tsopano tayesedwa olungama chifukwa chokhala ndi chikhulupiriro,+ tiyeni tikhale pa mtendere+ ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
9 Tsopano adzachita zoposa pamenepo mwa kutipulumutsa ku mkwiyo wake+ kudzera mwa Khristu, popeza tayesedwa olungama kudzera m’magazi a Khristuyo.+