1 Atesalonika 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kuyembekezera+ Mwana wake kuchokera kumwamba,+ amene anamuukitsa kwa akufa.+ Mwanayo ndi Yesu, amene akutipulumutsa ku mkwiyo ukubwerawo.+ 1 Atesalonika 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa Mulungu sanatisankhe kuti tidzaone mkwiyo.+ Anatisankha kuti tipeze chipulumutso+ kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+
10 ndi kuyembekezera+ Mwana wake kuchokera kumwamba,+ amene anamuukitsa kwa akufa.+ Mwanayo ndi Yesu, amene akutipulumutsa ku mkwiyo ukubwerawo.+
9 chifukwa Mulungu sanatisankhe kuti tidzaone mkwiyo.+ Anatisankha kuti tipeze chipulumutso+ kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+