Yesaya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ntchito ya chilungamo chenicheni idzakhala mtendere,+ ndipo zochita za chilungamo chenicheni zidzakhala bata ndi mtendere mpaka kalekale.+ Agalatiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+ Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+
17 Ntchito ya chilungamo chenicheni idzakhala mtendere,+ ndipo zochita za chilungamo chenicheni zidzakhala bata ndi mtendere mpaka kalekale.+
16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+
14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+