Salimo 72:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo. Salimo 119:165 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 165 Okonda chilamulo chanu amapeza mtendere wochuluka,+Ndipo palibe chowakhumudwitsa.+ Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+ Aroma 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera.
3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo.
12 “Pakuti anthu inu mudzachoka ndi chisangalalo+ ndipo mudzafika ndi mtendere.+ Mapiri ndi zitunda zidzakusangalalirani ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba m’manja.+
17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera.