Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+

      Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+

      Umenenso masamba ake safota,+

      Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+

  • Miyambo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+

  • Yesaya 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ntchito ya chilungamo chenicheni idzakhala mtendere,+ ndipo zochita za chilungamo chenicheni zidzakhala bata ndi mtendere mpaka kalekale.+

  • Yesaya 48:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+

  • 1 Akorinto 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pakuti Mulungu si Mulungu wachisokonezo,+ koma wamtendere.+

      Mofanana ndi m’mipingo yonse ya oyerawo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena