Deuteronomo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita nanu,+ ndi kuti musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+ Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+
23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita nanu,+ ndi kuti musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+
6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+