Yesaya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+ Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+