-
Hoseya 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Sindidzalanga ana anu aakazi chifukwa chakuti akuchita dama, kapenanso apongozi anu aakazi chifukwa chakuti akuchita chigololo, pakuti amuna akumatengana ndi mahule+ ndipo akumaperekera nsembe limodzi ndi mahule aakazi a pakachisi.+ N’chifukwa chake anthu osamvetsa zinthuwa adzapondedwapondedwa.+
-