Deuteronomo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+ Yesaya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+ Yeremiya 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Tsopano tamverani izi anthu opusa inu, anthu opanda nzeru mumtima mwanu,+ amene muli ndi maso koma simukuona,+ muli ndi makutu koma simukumva.+
6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+
9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+
21 “Tsopano tamverani izi anthu opusa inu, anthu opanda nzeru mumtima mwanu,+ amene muli ndi maso koma simukuona,+ muli ndi makutu koma simukumva.+