Deuteronomo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+ Yeremiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+
4 Koma Yehova sanakupatseni mtima woti muthe kuzindikira, maso oti muthe kuona ndi makutu oti muthe kumva, kufikira lero.+
22 Anthu anga ndi opusa.+ Iwo sanaganizire za ine.+ Iwo ndi ana opanda nzeru ndipo sazindikira kalikonse.+ Iwo ndi anzeru pa kuchita zoipa koma sadziwa kuchita zabwino.+