Salimo 119:165 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 165 Okonda chilamulo chanu amapeza mtendere wochuluka,+Ndipo palibe chowakhumudwitsa.+ Yesaya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+ Yesaya 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti Yehova wanena kuti: “Ndidzamupatsa mtendere ngati mtsinje+ ndi ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira,+ ndipo inu mudzayamwadi.+ Adzakunyamulani m’manja ndipo adzakusisitani mwachikondi atakuikani pamwendo.+
18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+
12 Pakuti Yehova wanena kuti: “Ndidzamupatsa mtendere ngati mtsinje+ ndi ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira,+ ndipo inu mudzayamwadi.+ Adzakunyamulani m’manja ndipo adzakusisitani mwachikondi atakuikani pamwendo.+