Yesaya 57:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno wina adzati, ‘Anthu inu, konzani msewu! Konzani msewu anthu inu! Lambulani msewu.+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”+ Mateyu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komabe pa iye yekha alibe mizu ndipo amapitirizabe kwa kanthawi. Koma pamene chisautso kapena mazunzo zayamba chifukwa cha mawuwo, iye amapunthwa mwamsanga.+ Aroma 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa. 1 Petulo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+
14 Ndiyeno wina adzati, ‘Anthu inu, konzani msewu! Konzani msewu anthu inu! Lambulani msewu.+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”+
21 Komabe pa iye yekha alibe mizu ndipo amapitirizabe kwa kanthawi. Koma pamene chisautso kapena mazunzo zayamba chifukwa cha mawuwo, iye amapunthwa mwamsanga.+
13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa.
6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+