Yesaya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+ 1 Akorinto 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pewani kukhala okhumudwitsa+ kwa Ayuda, ngakhalenso kwa Agiriki, ndi kwa mpingo wa Mulungu,
7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+