Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inu Mulungu wanga, ine ndikudziwa bwino kuti inu ndinu wosanthula mitima,+ ndiponso kuti mumakonda chilungamo.+ Ineyo kumbali yanga, ndapereka zinthu zonsezi mwaufulu ndi mtima wowongoka. Ndasangalala kuona anthu anu ali apawa, akupereka zopereka zawo mwaufulu kwa inu.

  • Yobu 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+

  • Salimo 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+

      Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+

  • Miyambo 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthu wolungama amayenda ndi mtima wosagawanika,+ ndipo ana ake amakhala odala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena