Ezekieli 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Amuna atatu awa: Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu,+ akanakhala m’dzikolo, iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+ Ezekieli 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ngakhale Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ akanakhala m’dzikolo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsamo mwana wawo wamwamuna kapena wamkazi. Iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+ Yakobo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawatcha odala.+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mwaona zimene Yehova anamupatsa,+ mwaona kuti Yehova ndi wachikondi chachikulu ndi wachifundo.+
14 “‘Amuna atatu awa: Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu,+ akanakhala m’dzikolo, iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+
20 ngakhale Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ akanakhala m’dzikolo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsamo mwana wawo wamwamuna kapena wamkazi. Iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+
11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawatcha odala.+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mwaona zimene Yehova anamupatsa,+ mwaona kuti Yehova ndi wachikondi chachikulu ndi wachifundo.+