Salimo 103:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachifundo ndi wachisomo,+Wosakwiya msanga ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, potengera Atate wanu amenenso ali wachifundo.+