Ezekieli 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ngakhale zikanakhala kuti Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ ali mʼdzikolo, iwo sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena aakazi. Iwo okhawo ndi amene akanapulumuka chifukwa ndi olungama.’”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
20 pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘ngakhale zikanakhala kuti Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ ali mʼdzikolo, iwo sakanapulumutsa ana awo aamuna kapena aakazi. Iwo okhawo ndi amene akanapulumuka chifukwa ndi olungama.’”+