Ezekieli 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ngakhale Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ akanakhala m’dzikolo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsamo mwana wawo wamwamuna kapena wamkazi. Iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
20 ngakhale Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ akanakhala m’dzikolo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsamo mwana wawo wamwamuna kapena wamkazi. Iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+