Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+

  • Salimo 26:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+

      Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+

  • Miyambo 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Munthu woyenda mowongoka mtima amaopa Yehova,+ koma munthu amene amayenda m’njira zokhotakhota amanyoza Mulungu.+

  • Mateyu 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndithu ndikukuuzani anthu inu, Mwa onse obadwa kwa akazi,+ sanabadwepo wamkulu woposa Yohane M’batizi. Koma munthu amene ali wocheperapo mu ufumu+ wakumwamba ndi wamkulu kuposa iyeyu.

  • Luka 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena