Salimo 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti mfumu imakhulupirira Yehova,+Imakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Wam’mwambamwamba. Iyo siidzagwedezeka.+ Salimo 37:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chilamulo cha Mulungu wake chili mumtima mwake.+Poyenda mapazi ake sadzaterereka.+ Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uzim’kumbukira m’njira zako zonse,+ ndipo iye adzawongola njira zako.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+
7 Pakuti mfumu imakhulupirira Yehova,+Imakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Wam’mwambamwamba. Iyo siidzagwedezeka.+