Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira+ kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukamenyane ndi Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”

  • 1 Samueli 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho Davide anafunsiranso kwa Yehova.+ Tsopano Yehova anamuyankha kuti: “Nyamuka, pita ku Keila, chifukwa ndikupereka Afilisitiwo m’manja mwako.”+

  • 1 Mbiri 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Ndipo iwe Solomo mwana wanga, dziwa+ Mulungu wa bambo wako, um’tumikire+ ndi mtima wathunthu+ ndi moyo wosangalala,+ chifukwa Yehova amasanthula mitima yonse+ ndipo amazindikira maganizo a munthu ndi zolinga zake zonse.+ Ukam’funafuna, adzalola kuti um’peze,+ koma ukam’siya+ adzakutaya kosatha.+

  • Nehemiya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aa, Yehova. Chonde, tcherani khutu ku pemphero la ine mtumiki wanu ndiponso pemphero+ la atumiki anu amene amasangalala ndi kuopa dzina lanu.+ Chonde, ndithandizeni ine mtumiki wanu kuti zinthu zindiyendere bwino lero+ ndipo mwamunayu andimvere chisoni.”+

      Pa nthawi imeneyi, ine ndinali woperekera chikho+ kwa mfumu.

  • Afilipi 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+

  • Akolose 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo chilichonse chimene mukuchita m’mawu kapena mu ntchito,+ muzichita zonse m’dzina la Ambuye Yesu,+ ndipo muziyamika+ Mulungu Atate kudzera mwa iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena