1 Mafumu 8:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.” 2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ Salimo 101:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzachita zinthu mwanzeru m’njira yowongoka.+Kodi inu mudzandithandiza liti?+Ndidzayendayenda m’nyumba yanga ndi mtima wanga wosagawanika.+
61 Mutumikire Yehova Mulungu wathu ndi mtima wathunthu+ mwa kuyenda motsatira malangizo ake ndi kusunga malamulo ake, monga mmene mukuchitira lero.”
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+
2 Ndidzachita zinthu mwanzeru m’njira yowongoka.+Kodi inu mudzandithandiza liti?+Ndidzayendayenda m’nyumba yanga ndi mtima wanga wosagawanika.+