2 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anayankha kuti: “Pamene mwana anali ndi moyo ndinali kusala kudya+ ndipo ndinali kulira+ chifukwa mumtima mwanga ndinali kunena kuti, ‘Angadziwe ndani, mwina Yehova angandikomere mtima ndipo mwanayu angakhale ndi moyo?’+ Yesaya 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapemphera kuti: “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+
22 Iye anayankha kuti: “Pamene mwana anali ndi moyo ndinali kusala kudya+ ndipo ndinali kulira+ chifukwa mumtima mwanga ndinali kunena kuti, ‘Angadziwe ndani, mwina Yehova angandikomere mtima ndipo mwanayu angakhale ndi moyo?’+
3 Iye anapemphera kuti: “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+