Yesaya 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pita, kauze Hezekiya kuti, ‘Yehova Mulungu wa Davide kholo lako+ wanena kuti: “Ndamva pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Tsopano ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako.+ Yoweli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu? Amosi 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+ Yona 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+
5 “Pita, kauze Hezekiya kuti, ‘Yehova Mulungu wa Davide kholo lako+ wanena kuti: “Ndamva pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Tsopano ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako.+
14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu?
15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+
9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+