Ekisodo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa tsiku lotsatira, Mose anati kwa anthuwo: “Inuyo mwachita tchimo lalikulu.+ Choncho ndikwera kupita kwa Yehova kuti mwina ndikakam’chonderera angakukhululukireni tchimo lanu.”+ Salimo 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
30 Pa tsiku lotsatira, Mose anati kwa anthuwo: “Inuyo mwachita tchimo lalikulu.+ Choncho ndikwera kupita kwa Yehova kuti mwina ndikakam’chonderera angakukhululukireni tchimo lanu.”+
12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+