Genesis 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimene zinali kulowazo, zazimuna ndi zazikazi zamtundu uliwonse, zinalowa monga mmene Yehova anamulamulira Nowa. Kenako Yehova anatseka chitseko.+ Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+ Yesaya 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+
16 Zimene zinali kulowazo, zazimuna ndi zazikazi zamtundu uliwonse, zinalowa monga mmene Yehova anamulamulira Nowa. Kenako Yehova anatseka chitseko.+
20 Mudzawabisa m’malo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa pamaso pa anthu amene asonkhana pamodzi kuti awachitire chiwembu.+Mudzawabisa mumsasa wanu kwa anthu ofuna kukangana nawo.+
20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+