Salimo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+ Salimo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.] Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.
5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+
7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.]
19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.