Salimo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+ Salimo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+ Salimo 119:114 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 114 Inu ndinu malo anga obisalamo ndi chishango changa,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+
9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+
5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+