Salimo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma inu Yehova ndinu chishango changa,+Ulemerero wanga+ ndiponso Wonditukula mutu.+ Salimo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.] Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+
7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.]
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+