Salimo 119:81 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Ine ndafooka chifukwa cholakalaka chipulumutso chanu,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+ Salimo 130:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+
5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+