Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+

  • Salimo 27:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+

      Yembekezera Yehova.+

  • Salimo 33:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Moyo wathu wakhala ukuyembekeza Yehova.+

      Iye ndi mthandizi wathu ndi chishango chathu.+

  • Salimo 40:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+

      Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+

  • Yesaya 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine ndiziyembekezera Yehova,+ amene wabisira nkhope yake nyumba ya Yakobo,+ ndipo ndithu ndiziyembekezera iyeyo.+

  • Yesaya 26:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Inu Yehova, ife tayembekezera inu pofunafuna njira yanu ya chilungamo.+ Mtima wathu wakhala ukulakalaka kuti ukumbukire dzina lanu, ndi zimene dzinalo limaimira.+

  • Luka 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena