Salimo 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+ Salimo 130:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+
6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+