Salimo 62:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithudi, yembekezera Mulungu modekha, iwe moyo wanga,+Chifukwa chiyembekezo changa chichokera kwa iye.+ Salimo 130:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+ Aroma 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu amene amapereka chiyembekezo akudzazeni ndi chimwemwe chonse ndi mtendere wonse chifukwa cha kukhulupirira kwanu, kuti mukhale ndi chiyembekezo chachikulu mwa mphamvu ya mzimu woyera.+
5 Ndithudi, yembekezera Mulungu modekha, iwe moyo wanga,+Chifukwa chiyembekezo changa chichokera kwa iye.+
5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+
13 Mulungu amene amapereka chiyembekezo akudzazeni ndi chimwemwe chonse ndi mtendere wonse chifukwa cha kukhulupirira kwanu, kuti mukhale ndi chiyembekezo chachikulu mwa mphamvu ya mzimu woyera.+