Salimo 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani ukutaya mtima, moyo wangawe?+Ndipo n’chifukwa chiyani ukusautsika mkati mwanga?Yembekezera Mulungu,+Ndipo ndidzamutamanda pakuti iye ndiye mpulumutsi wanga wamkulu ndi Mulungu wanga.+ Salimo 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
5 N’chifukwa chiyani ukutaya mtima, moyo wangawe?+Ndipo n’chifukwa chiyani ukusautsika mkati mwanga?Yembekezera Mulungu,+Ndipo ndidzamutamanda pakuti iye ndiye mpulumutsi wanga wamkulu ndi Mulungu wanga.+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+