Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Choncho dziwani kuti Yehova adzapatula wokhulupirika wake.+

      Yehova adzamva ndikaitana.+

  • Salimo 40:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+

      Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+

  • Salimo 65:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+

  • Yesaya 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+

  • Yesaya 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 M’tsiku limenelo munthu adzati: “Taonani! Uyu ndiye Mulungu wathu.+ Chiyembekezo chathu chinali mwa iye+ ndipo iye watipulumutsa.+ Uyu ndi Yehova.+ Chiyembekezo chathu chinali mwa iye. Tiyeni tisangalale ndi kukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa iye.”+

  • 1 Yohane 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena