Ekisodo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu ananenanso kwa Mose kuti: “Ine ndine Yehova.+ Salimo 97:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri anasungunuka ngati phula chifukwa cha Yehova,+Chifukwa cha Ambuye wa dziko lonse lapansi.+ Zefaniya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+
12 Mwa iwe ndidzasiyamo anthu ena, odzichepetsa ndi ofatsa,+ ndipo amenewa adzapeza chitetezo m’dzina la Yehova.+