Salimo 97:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri amasungunuka ngati phula pamaso pa Yehova,+Pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi.