Salimo 97:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri anasungunuka ngati phula chifukwa cha Yehova,+Chifukwa cha Ambuye wa dziko lonse lapansi.+