Genesis 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+ Miyambo 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usanene kuti: “Ndidzabwezera choipa.”+ Khulupirira Yehova+ ndipo iye adzakupulumutsa.+ Luka 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa maso anga aona njira yanu yopulumutsira+