Yesaya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova waika pamtunda dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione,+ ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona chipulumutso cha Mulungu wathu.+ Luka 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse adzaona njira ya Mulungu yopulumutsira.’”+ Machitidwe 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+
10 Yehova waika pamtunda dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione,+ ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona chipulumutso cha Mulungu wathu.+
12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+