Mateyu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+ Machitidwe 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa m’dzina lake.”+ Afilipi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+
21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+
43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa m’dzina lake.”+
9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+