Aroma 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Paja Lemba limati: “Palibe wokhulupirira iye,+ amene adzakhumudwe.”+ Agalatiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Malemba+ anatsekera zinthu zonse n’kuziika pansi pa uchimo,+ kuti lonjezolo, limene limakhalapo mwa kukhulupirira Yesu Khristu, liperekedwe kwa okhulupirirawo.+
22 Koma Malemba+ anatsekera zinthu zonse n’kuziika pansi pa uchimo,+ kuti lonjezolo, limene limakhalapo mwa kukhulupirira Yesu Khristu, liperekedwe kwa okhulupirirawo.+