Salimo 98:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+ Yesaya 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Yesaya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova waika pamtunda dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione,+ ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona chipulumutso cha Mulungu wathu.+ Luka 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa maso anga aona njira yanu yopulumutsira+ Machitidwe 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+
2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+
5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+
10 Yehova waika pamtunda dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione,+ ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona chipulumutso cha Mulungu wathu.+
28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+