Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yehova wa makamu adzakwezeka kudzera m’chiweruzo,+ ndipo Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera m’chilungamo.+

  • Yesaya 60:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+ ndipo mafumu+ adzatsata kunyezimira kwako.+

  • Yesaya 62:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako+ mkazi iwe,+ ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzatchedwa ndi dzina latsopano+ limene pakamwa pa Yehova padzasankhe.

  • Aroma 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mulungu anam’pereka monga nsembe yachiyanjanitso,+ mwa kukhala ndi chikhulupiriro m’magazi ake.+ Mulungu anachita izi pofuna kuonetsa chilungamo chake pokhululuka machimo+ amene anachitika kale, pamene iye anali kusonyeza khalidwe losakwiya msanga,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena