Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano mantha+ a Yehova akugwireni.+ Samalani mmene mukuchitira+ chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+ Salimo 98:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
7 Tsopano mantha+ a Yehova akugwireni.+ Samalani mmene mukuchitira+ chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+
2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+