Deuteronomo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+ Yobu 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+ Aroma 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe, ngati kulungama kwa Mulungu+ kukuonekera chifukwa cha kusalungama kwathu, ndiye tinene kuti chiyani? Kodi tingati Mulungu ndi wosalungama+ poonetsa mkwiyo wake? (Ndikulankhula mmene anthu+ amalankhulira.)
16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+
10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+
5 Komabe, ngati kulungama kwa Mulungu+ kukuonekera chifukwa cha kusalungama kwathu, ndiye tinene kuti chiyani? Kodi tingati Mulungu ndi wosalungama+ poonetsa mkwiyo wake? (Ndikulankhula mmene anthu+ amalankhulira.)