Salimo 98:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wachititsa kuti chipulumutso chake chidziwike.+Wachititsa kuti anthu a mitundu yonse aone chilungamo chake.+
2 Yehova wachititsa kuti chipulumutso chake chidziwike.+Wachititsa kuti anthu a mitundu yonse aone chilungamo chake.+