Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Salimo 92:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuti alengeze kuti Yehova ndi wolungama.+Iye ndi Thanthwe langa,+ ndipo sachita zosalungama.+ Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+ Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+