Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+ Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+ Yeremiya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Kodi wanzeru ndani kuti amvetse zimenezi, kapenanso ndani amene Yehova wamulankhula kuti anene zimenezi?+ N’chifukwa chiyani dzikoli lidzawonongedwa ndiponso kutenthedwa n’kukhala ngati chipululu chopanda munthu wodutsamo?”+
43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+
12 “Kodi wanzeru ndani kuti amvetse zimenezi, kapenanso ndani amene Yehova wamulankhula kuti anene zimenezi?+ N’chifukwa chiyani dzikoli lidzawonongedwa ndiponso kutenthedwa n’kukhala ngati chipululu chopanda munthu wodutsamo?”+