Yesaya 42:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndani pakati panu amene adzamvetsere zinthu zimenezi? Ndani adzatchere khutu ndi kumvetsera zinthu zimene zidzamuthandize m’tsogolo?+ Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
23 Ndani pakati panu amene adzamvetsere zinthu zimenezi? Ndani adzatchere khutu ndi kumvetsera zinthu zimene zidzamuthandize m’tsogolo?+
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+